03/07/2024
ABWENZI ADZIKO LAPANSI
chapter 16
LYDEN, »dzidzidzi heiiii
kod umamwa madiragi..?
BWANJI ukuyankhura
Nonsense...? mesa iwe
Ndi amene wativulaza ife
Watibaya jekeseni....?😳🙊
Ndiwe chitsilu LYDEN
Ndipo ndipita ku police
Heiiii ndinakulakwilani
chani anthu inu...?
kundicheka chonchi
chifukwa chani....?
mwandicheka ndi
kumaliseche komwe
ndalakwa chani ine...?😭
ma doctor, »anayamba
kukokana kokana nawo
aPOLICE anatulukira ku
chipatala kuja ndi mabuku
“NTHAWI imeneyi mabuku
anali mu Unyoro....🥺
Edina, »chokha chongoti
Mabuku thaaa amvekere
Heiiii sir munthu wina ndi
Uyu amene amafunanso
kundigwililira winayo akuti
ndi Mark analipo anthu
atatu omwe amafuna
kundipanga chipongwe
ine...😭 💔 mwamwai
ndinakwanitsa kuthawa...💔😭
“aPOLICE, »anagwira
khosi la mabuku
amvekere ifetu timadziwa
kuti iweyo ndiye mwini
Film ndeno chimene
wapanga ndichani...?
kucheka tsikana moyipa
chonchi...?😏 ndiwe otani
nkhanza kupangila tsikana
Ngati Uyu...?
Mabuku, »anayamba
kulira milomo imangonjanja
kusowa choyankhula...😭 💔
SINE OLAKWA INE...😭 💔
NTHAWI YOMWEYO
Panatulukira mark pa
malowa ali pa wirotcheya
akumuyendetsa ndi Stella
Edina, »anangoti mark
thaaa amvekere ehee
INSPECTOR munthu wina
ndi Uyu, »Uyu nde tinafika
POLIMBANA ndi amene
anandicheka kumaliseche
mwamwayi ndinamulanda
mfuti ndikumuwombera
pa mtima...😭 💔
“Mark, »anayamba
kuzaza diso lili pa
nthunda amvekere...😂🤣
IKANI GAWO 16😁😹
mawa 8:00AM
ikuyambika..🥳🥳